Ashahadu

Ashahadu God don't have child

05/01/2025

Ndipo musakayike imfa ik*tidikila ,manda ak*tidikilaso ,angele amafuso akudikilaso ,mphusi zik*tidikla ,zosezitu apa ndimasauso owonekela ,,udandaulileni Moyo wanu ndipo ziganizileni k*t kod zikandithala bwanji manda ,ndipo Allah akulakhula mu Qur'an

وَجَاءَتْ سَكْرَةُ الْمَوْتِ بِالْحَقِّ ۖ ذَ‌ٰلِكَ مَا كُنتَ مِنْهُ تَحِيدُ Ndipo kuledzera kwa imfa kukam'dzera Mwa choona, (pamenepo adzauzidwa): 'Ichi ndi chomwe mumachithawa chija.',,,,,,

Ndithudi ili ndsku lamasauso kwa anthu osasamala swalah ndizintchto zina zabwino ,,,,,,,,,
Ndipo musaone ngat Allah sali nanu pafupi ,,gwilani ntchito iliyoseyo ndipo Angelo akulemba choipa(or zolakhula zanu samalani) ,or chabwino ndipo sapanga mistake

مَّا يَلْفِظُ مِن قَوْلٍ إِلَّا لَدَيْهِ رَقِيبٌ عَتِيدٌ
Palibe chilichonse chimene Amayankhula koma pafupi ndi iye pali Mlonda amene wakonzekera (kulemba).

03/01/2025

M***a kupanga chizake ndi Allah ngati mungasate malamulo ake ,ndikuwasamala ndipo muzasangalala forever

31/12/2024

Muzikhulupilila k*t chifukwa cha nthawi zinthu zimasitha. Mukhulupililen Allah

22/12/2024

Mene mukugwilila ntchitomo ndikumapeza kenakake ndikambili kameneko pang'onopang'o ndipo zizatheka(InshaAllah)

20/12/2024

Fear NOT, But Fear DEATH!

20/12/2024

Address

Malawi, In Machinga , Mbanila
Johannesburg

Telephone

+27834957766

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ashahadu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share

Category